05/06/2026
Week 1 ya June ija yatha motere
Sunbird wasungabe chinthuchi
Real life talk | Money & daily struggles 🇲🇼
Best investment Relatable content every day Follow for more
05/06/2026
Week 1 ya June ija yatha motere
Sunbird wasungabe chinthuchi
05/06/2026
Long term ija
Omwe agula ma share and akhala nawo kwa Chaka ngakhale ena akulira iwo angoti owowo
Chifukwa even ma share price wo atsika koma pomwe anagulirira iwo ali kutali
Mwezi ngati omweuno
Share ya FMBCH inali pa K904
Yatsika pano ili pa K1 648
Ndekuti akadalibe ndi phindu loposa 74%
Standard bank inali pa 1 sau nkanthu pano yatsika ikadali pa 3 sau nkanthu still 70% gain
NBS inali pa K335 lero ili pa 742 over 120% gain
Yanu yapanga loss zingati since June last year?
Kapena since June last year? mwapanga gain zingati?
Image: Daily summary ya pa 5 June 2025
Pa Mainboard Unofficially
CDH
MAIIC
Centenary
04/06/2026
Always With You
04/06/2026
Ma tally
FDH Financial Holdings has disclosed that its newly acquired Mozambique business is yet to start contributing to the group's earnings.
Managing Director, Noel Nkulichi, has disclosed during the company's 19th Annual General Meeting in Blantyre, where he said the Mozambican subsidiary has remained loss-making due to regulatory restrictions that had been imposed on the institution before its acquisition.
He, however, said the company has already embarked on a turnaround strategy aimed at restoring the bank to profitability so that it can begin contributing positively to the group's financial performance.
FDH Acquired 98.87% stake in Ecobank Mozambique, which now operates as FDH Mozambique SA.
By Earlene Chimoyo
Ma shareholders a OMU suti timakusalani ai inu ndi ma bigger
OMU bho?
04/06/2026
Company imapanga declare dividends ngati company yo yapanga phindu and ili ndi cash pa phindu lapangalo
Health ya company imaoneka pomwe ikupitiliza kupereka ma dividends regularly
Health ya company sioneka pomwe share price ikutsika kapena kukwera kwambiri
Izitu nchifukwa chake Ma company akupitilizabe kugawa ma dividends ngakhale ma price a share yawo akutsika
Inu mubazifunsapo kuti
Why?
Ngati company ikugwa ingamagaweso phindu?
FDHB plc Shareholders
Lero waku Mpemba tikakumane kumeko tikudziwana
03/06/2026
Dividend nkuzakwera ndi 128.6%
Ndalama zikupangidwa
Sugar sugar
03/06/2026
Tawerukako NITL pa front apo
NBM nayo mbuyomo